Zamkatimu
June 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
AUGUST 4-10, 2014
“Uzikonda Yehova Mulungu Wako”
TSAMBA 12 • NYIMBO: 3, 65
AUGUST 11-17, 2014
“Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondera Wekha”
TSAMBA 17 • NYIMBO: 84, 72
AUGUST 18-24, 2014
Kodi Mumaona Anthu Ofooka Mmene Yehova Amawaonera?
TSAMBA 23 • NYIMBO: 77, 79
AUGUST 25-31, 2014
Thandizani Ena Kuti Azichita Zonse Zimene Angathe
TSAMBA 28 • NYIMBO: 42, 124
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ “Uzikonda Yehova Mulungu Wako”
▪ “Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondera Wekha”
Nkhani ziwirizi zikufotokoza malamulo awiri aakulu a m’Chilamulo amene Yesu Khristu ananena. Onani zimene Yesu ankatanthauza ponena kuti tizikonda Yehova ndi mtima wathu wonse, moyo wathu wonse komanso maganizo athu onse. Onaninso mmene tingasonyezere kuti timakonda anzathu mmene timadzikondera.
▪ Kodi Mumaona Anthu Ofooka MmeneYehova Amawaonera?
▪ Thandizani Ena Kuti Azichita ZonseZimene Angathe
Kodi tingathandize bwanji anthu amene afooka? Nkhani yoyamba ikuyankha funso limeneli. Nkhani yachiwiri ikufotokoza zimene tingachite pothandiza abale achinyamata komanso atsopano kuti azichita zonse zimene angathe.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 “Salaza Njira ya Phazi Lako” Kuti Uyende Bwino
7 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
8 Kodi Tingathandize Bwanji Akhristu Amene Banja Lawo Latha?
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira kwa msodzi wolankhula Chimbukushu m’mphepete mwa mtsinje wa Okavango
BOTSWANA
KULI ANTHU
2,021,000
KULI OFALITSA
2,096
KULI MIPINGO
47
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO MU 2013
5,735