Zamkatimu
July 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
SEPTEMBER 1-7, 2014
TSAMBA 7 • NYIMBO: 63, 66
SEPTEMBER 8-14, 2014
Anthu a Yehova Amakana Kuchita Zosalungama
TSAMBA 12 • NYIMBO: 64, 61
SEPTEMBER 15-21, 2014
TSAMBA 23 • NYIMBO: 31, 92
SEPTEMBER 22-28, 2014
TSAMBA 28 • NYIMBO: 102, 103
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ “Yehova Amadziwa Anthu Ake”
▪ Anthu a Yehova Amakana Kuchita Zosalungama
Nkhanizi zikufotokoza tanthauzo la lemba la 2 Timoteyo 2:19. Zikusonyezanso kuti lembali likugwirizana ndi zimene zinachitika m’nthawi ya Mose. Zitithandiza kudziwa mmene tingasonyezere kuti ndife ‘anthu a Yehova’ ndiponso kuti timakana kuchita zosalungama.
▪ “Inu Ndinu Mboni Zanga”
▪ “Mudzakhala Mboni Zanga”
M’nkhanizi tiona chifukwa chake timatchedwa Mboni za Yehova. Tiyenera kuchita khama pa ntchito yolalikira za Yehova ndi Yesu komanso kukhala ndi khalidwe loyera limene limawalemekeza.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
PATSAMBA LOYAMBA: Alongo awiri akugwiritsa ntchito buku la Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? polalikira azimayi awiri achindewele. Azimayiwa avala mmene Andewele amavalira ndipo nyumbayo ndi mmene nyumba za kumidzi yawo zimaonekera. Ku South Africa, anthu awiri okha pa anthu 100 alionse ndi Andewele
SOUTH AFRICA
KULI ANTHU
50,500,000
KULI OFALITSA
94,101
OFALITSA OLANKHULA CHINDEWELE
1,003