Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w14 11/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2014
  • Timitu
  • MAGAZINI YOPHUNZIRA
  • NKHANI ZOPHUNZIRA
  • M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
Nsanja ya Olonda—2014
w14 11/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

November 15, 2014

© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

MAGAZINI YOPHUNZIRA

DECEMBER 29, 2014–JANUARY 4, 2015

Kodi Kuuka kwa Yesu Kumatithandiza Bwanji?

TSAMBA 3 • NYIMBO: 5, 60

JANUARY 5-11, 2015

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Oyera?

TSAMBA 8 • NYIMBO: 119, 17

JANUARY 12-18, 2015

Tikhale Oyera M’makhalidwe Athu Onse

TSAMBA 13 • NYIMBO: 65, 106

JANUARY 19-25, 2015

“Anthu Amene Mulungu Wawo Ndi Yehova”

TSAMBA 18 • NYIMBO: 46, 63

JANUARY 26, 2015–FEBRUARY 1, 2015

“Tsopano Ndinu Mtundu wa Anthu a Mulungu”

TSAMBA 23 • NYIMBO: 112, 101

NKHANI ZOPHUNZIRA

▪ Kodi Kuuka kwa Yesu Kumatithandiza Bwanji?

Nkhaniyi ikufotokoza umboni wotitsimikizira kuti Yesu anaukitsidwa ndipo adakali moyo. Kudziwa zimenezi kungatilimbikitse ndiponso kutithandiza pa ntchito yathu yolalikira.

▪ N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Oyera?

▪ Tikhale Oyera M’makhalidwe Athu Onse

Nkhanizi zikuchokera m’buku la Levitiko ndipo zikuyankha mafunso awa: N’chifukwa chiyani Yehova amafuna kuti tizikhala oyera? Kodi tingakhale bwanji oyera? Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife oyera m’makhalidwe athu onse?

▪ “Anthu Amene Mulungu Wawo Ndi Yehova”

▪ “Tsopano Ndinu Mtundu wa Anthu a Mulungu”

Anthu ena amene timaphunzira nawo Baibulo sakhulupirira kuti Yehova ali ndi gulu limodzi padzikoli. Iwo amaganiza kuti munthu wa m’chipembedzo chilichonse akhoza kusangalatsa Mulungu ngati akumulambira mochokera pansi pa mtima. Nkhanizi zikusonyeza kuti munthu ayenera kuzindikira anthu a Mulungu ndiponso kugwirizana nawo pomutumikira.

M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI

28 Mafunso Ochokera kwa Owerenga

31 Kale Lathu

PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira mumzinda waukulu wa Santiago de Cuba. Mzindawu uli pachilumba cha Cuba chomwe chimadziwika ndi nyimbo komanso magule

CUBA

KULI ANTHU

11,163,934

KULI OFALITSA

96,206

KULI APAINIYA OKHAZIKIKA

9,040

Ofalitsa amene ali ndi vuto losamva ndipo amagwiritsa ntchito chinenero chamanja cha ku Cuba alipo 270
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena