Zamkatimu
February 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
APRIL 6-12, 2015
Khalani Odzichepetsa Ndiponso Achifundo Ngati Yesu
TSAMBA 5 • NYIMBO: 5, 84
APRIL 13-19, 2015
Khalani Olimba Mtima Ndiponso Ozindikira Ngati Yesu
TSAMBA 10 • NYIMBO: 99, 108
APRIL 20-26, 2015
Zinthu Zimene Zinathandiza Kuti Anthu Aphunzire za Yehova
TSAMBA 19 • NYIMBO: 98, 104
APRIL 27, 2015–MAY 3, 2015
Yehova Akutsogolera Ntchito Yolalikira Padziko Lonse
TSAMBA 24 • NYIMBO: 103, 66
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Khalani Odzichepetsa Ndiponso Achifundo Ngati Yesu
▪ Khalani Olimba Mtima Ndiponso Ozindikira Ngati Yesu
Baibulo limatilimbikitsa kutsatira mapazi a Yesu mosamala. (1 Pet. 2:21) Koma kodi anthu ochimwafe tingatsatiredi chitsanzo cha Yesu? Nkhani yoyamba ikufotokoza zimene tingachite kuti tikhale odzichepetsa ndiponso achifundo ngati Yesu. Nkhani yachiwiri ikusonyeza zimene tingachite kuti tikhale olimba mtima ndiponso ozindikira ngati Yesu.
▪ Zinthu Zimene Zinathandiza Kuti Anthu Aphunzire za Yehova
▪ Yehova Akutsogolera Ntchito Yolalikira Padziko Lonse
Nkhani yoyamba ikusonyeza zimene Yehova anachita pothandiza Akhristu oyambirira kuti azilalikira uthenga wabwino. M’nkhani yachiwiri tidzakambirana zinthu za masiku ano zimene zimatithandiza kuti tizilalikira uthenga wa Ufumu kwa anthu amtima wabwino padziko lonse lapansi.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 Anthu a ku Japan Analandira Mphatso
15 Kodi Tingatani Kuti Tizikondabe Kulalikira?
29 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira kunyumba ndi nyumba pachilumba cha Bali ndipo akugawira Galamukani! kwa munthu amene wawalandira bwino
INDONESIA
KULI ANTHU
237,600,000
KULI OFALITSA
24,521
KULI APAINIYA OKHAZIKIKA
2,472
Apainiya apadera 369 akutumikira m’zilumba 28 za m’dzikoli