Zamkatimu
March 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
MAY 4-10, 2015
“Munavomereza Kuti Zimenezi Zichitike”
TSAMBA 7 • NYIMBO: 65, 64
MAY 11-17, 2015
TSAMBA 12 • NYIMBO: 108, 24
MAY 18-24, 2015
Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Fanizo la Matalente?
TSAMBA 19 • NYIMBO: 101, 116
MAY 25-31, 2015
Tizithandiza Abale a Khristu Mokhulupirika
TSAMBA 25 • NYIMBO: 107, 63
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ “Munavomereza Kuti Zimenezi Zichitike”
▪ Kodi ‘Mudzakhalabe Maso’?
Nkhani yoyamba ikufotokoza kuti Yehova akutsogolera anthu powaphunzitsa m’njira yosavuta. Nkhani yachiwiri ikufotokoza fanizo la Yesu la anamwali 10. Fanizoli lingatithandize kukhalabe maso masiku ano.
▪ Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Fanizo la Matalente?
▪ Tizithandiza Abale a Khristu Mokhulupirika
Nkhanizi zikufotokoza mafanizo awiri amene Yesu anapereka pofotokoza chizindikiro cha kukhalapo kwake. Fanizo limodzi ndi lokhudza akapolo amene anapatsidwa matalente ndipo lina ndi loti anthu adzasiyanitsidwa ngati nkhosa ndi mbuzi. M’nkhanizi tiziyankha funso lakuti: N’chifukwa chiyani Yesu anapereka fanizoli ndipo likutithandiza bwanji?
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 Tinapeza Ntchito Yabwino Kwambiri
17 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
30 Kodi N’zothekadi Kukwatira Kapena Kukwatiwa “Mwa Ambuye”?
PATSAMBA LOYAMBA: Anthu ambiri amapita ku Honduras kukaona mabwinja a ku Copán ndipo a Mboni za Yehova akuthandiza anthuwa kuti aziganizira zam’tsogolo
HONDURAS
KULI ANTHU
8,111,000
KULI OFALITSA
22,098
KULI APAINIYA OKHAZIKIKA
3,471
M’dzikoli, anthu ambiri amalankhula Chisipanishi. Koma kuli ofalitsa 365 m’mipingo 12 amene amagwiritsa ntchito chilankhulo cha Chigarifuna. Chilankhulo chamanja cha kumeneko chimagwiritsidwanso ntchito m’mipingo 11 ndi timagulu titatu