Zamkatimu
April 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
JUNE 1-7, 2015
Kodi Mumaphunzitsa Ena Kuti Akhalenso Akulu?
TSAMBA 3 • NYIMBO: 123, 121
JUNE 8-14, 2015
Zimene Mungachite Pophunzitsa Ena Kuti Akhale Akulu
TSAMBA 9 • NYIMBO: 45, 70
JUNE 15-21, 2015
Kodi Yehova Ndi Mnzanu Weniweni?
TSAMBA 19 • NYIMBO: 91, 11
JUNE 22-28, 2015
Muzikhulupirira Yehova Nthawi Zonse
TSAMBA 24 • NYIMBO: 106, 49
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Kodi Mumaphunzitsa Ena Kuti Akhalenso Akulu?
▪ Zimene Mungachite Pophunzitsa Ena Kuti Akhale Akulu
N’chifukwa chiyani akulu ayenera kuphunzitsa ena kuti akhalenso akulu? Kodi angawaphunzitse bwanji? Kodi akulu komanso anthu amene akuphunzitsidwawo angaphunzire chiyani kwa Samueli, Eliya ndiponso Elisa? Nkhani ziwirizi ziyankha mafunso amenewa.
▪ Kodi Yehova Ndi Mnzanu Weniweni?
▪ Muzikhulupirira Yehova Nthawi Zonse
Ubwenzi wabwino ndi Yehova ungatithandize kuti tipirire vuto lililonse. Nkhani ziwirizi zikusonyeza zimene tingachite kuti tikhale pa ubwenzi wabwino ndi Yehova. Choyamba tiyenera kulankhulana naye ndipo chachiwiri tiyenera kumukhulupirira nthawi zonse.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
14 Ndadalitsidwa “M’nthawi Yabwino ndi M’nthawi Yovuta”
PATSAMBA LOYAMBA: Mkulu akuphunzitsa m’bale kulalikira pogwiritsa ntchito shelefu yamatayala m’mphepete mwa msewu wa Haiphong ku Kowloon
HONG KONG
KULI ANTHU
7,234,800
KULI OFALITSA
5,747
MAPHUNZIRO A BAIBULO
6,382
180,000+
Gulu limapeza zinthu monga mashelefu ndi matebulo zoposa 180,000 kudzera ku ofesi ya nthambi ya ku Hong Kong n’kutumiza m’mayiko osiyanasiyana