Zamkatimu
May 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
JUNE 29, 2015–JULY 5, 2015
Khalani Maso, Satana Akufuna Kukumezani
TSAMBA 9 • NYIMBO: 54, 43
JULY 6-12, 2015
TSAMBA 14 • NYIMBO: 60, 100
JULY 13-19, 2015
TSAMBA 19 • NYIMBO: 81, 134
JULY 20-26, 2015
Tsanzirani Amene Wakulonjezani Moyo Wosatha
TSAMBA 24 • NYIMBO: 12, 69
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Khalani Maso, Satana Akufuna Kukumezani
▪ N’zotheka Kugonjetsa Satana
M’Baibulo, Satana amayerekezeredwa ndi mkango wobangula umene ukufunafuna nyama. Iye ndi wamphamvu, wolusa komanso wachinyengo. Nkhanizi zikusonyeza kuti tiyenera kusamala kwambiri kuti asativulaze. Itithandizanso kudziwa zimene tiyenera kuchita kuti titetezeke ku misampha yake.
▪ Ankaona Malonjezo Ali Patali
▪ Tsanzirani Amene Wakulonjezani Moyo Wosatha
Anthufe tili ndi luso lotha kuona m’maganizo mwathu zinthu zimene sitinazionepo. Luso limeneli tikhoza kuligwiritsa ntchito mwanzeru kapena mopanda nzeru. M’nkhanizi tiona zimene tingaphunzire kwa anthu angapo otchulidwa m’Baibulo. Tiona mmene tingagwiritsire ntchito luso loona zinthu m’maganizo mwathu kuti titsanzire makhalidwe a Yehova monga chikondi, chifundo, nzeru ndi chimwemwe.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 Chikondi Changa cha Poyamba Chandithandiza Kupirira
29 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Abale awiri akuchititsa phunziro la Baibulo
ARMENIA
KULI ANTHU
3,026,900
KULI OFALITSA
11,143
APAINIYA OKHAZIKIKA
2,205
23,844
Opezeka pa Chikumbutso pa April 14, 2014. Anthuwa ndi ambiri tikayerekezera ndi chiwerengero cha ofalitsa