Zamkatimu
August 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
SEPTEMBER 28, 2015–OCTOBER 4, 2015
Tiziganizira Kwambiri Chikondi cha Yehova
TSAMBA 9
OCTOBER 5-11, 2015
TSAMBA 14
OCTOBER 12-18, 2015
Tizikonzekera Moyo wa M’dziko Latsopano
TSAMBA 19
OCTOBER 19-25, 2015
Tizisankha Mwanzeru Anthu Ocheza Nawo M’masiku Otsiriza Ano
TSAMBA 24
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Tiziganizira Kwambiri Chikondi cha Yehova
Nthawi zonse Yehova amasonyeza chikondi kwa anthu ake. Nkhaniyi ikufotokoza zimene Mulungu wachita posonyeza chikondicho. Kuganizira mfundo yakuti Yehova amakukondani kungakuthandizeni kukhala naye pa ubwenzi wolimba.
▪ Tiziyembekezerabe
▪ Tizikonzekera Moyo wa M’dziko Latsopano
Nthawi ikamadutsa tisamaganize kuti malonjezo a Mulungu sadzakwaniritsidwa. Pali zifukwa zomveka zoti tizikhulupirira kuti adzakwaniritsidwadi. Nkhanizi zikufotokoza zimene tingachite kuti tiziyembekezerabe.
▪ Tizisankha Mwanzeru Anthu Ocheza Nawo M’masiku Otsiriza Ano
N’chifukwa chiyani tiyenera kusankha mwanzeru anthu ocheza nawo m’masiku otsiriza ano? Kodi Mawu a Mulungu angatithandize bwanji kuchita zimenezi? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 “Zilumba Zambiri Zisangalale”
29 Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Chitsanzo cha Jowana?
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: M’bale wachinyamata akusonyeza mnyamata mnzake vidiyo ya pa jw.org mumzinda wa Esperanza
ARGENTINA
KULI ANTHU
42,670,000
KULI OFALITSA
150,171
KULI APAINIYA OKHAZIKIKA
18,538
MAPHUNZIRO A BAIBULO
126,661
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO MU (2014)