Zamkatimu
October 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
NOVEMBER 30, 2015–DECEMBER 6, 2015
Kodi Mumaona Dzanja la Mulungu Likukuthandizani?
TSAMBA 4
DECEMBER 7-13, 2015
“Tiwonjezereni Chikhulupiriro”
TSAMBA 9
DECEMBER 14-20, 2015
Tisalole Chilichonse Kutisokoneza Potumikira Yehova
TSAMBA 18
DECEMBER 21-27, 2015
Tiziganizira Kwambiri za Yehova
TSAMBA 23
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Kodi Mumaona Dzanja la Mulungu Likukuthandizani?
▪ “Tiwonjezereni Chikhulupiriro”
M’nkhani yoyamba tikambirana umboni woti Yehova amatikonda komanso kutithandiza. Zimenezi zitithandiza kuti tisakhale ngati anthu amene amalakwitsa zinthu chifukwa chosazindikira zimene Yehova akuchita. Nkhani yachiwiri ikusonyeza kuti chikhulupiriro n’chofunika kwambiri kuti tidzapulumuke ndipo tikambirana zimene tingachite kuti tikhale ndi chikhulupiriro cholimba.—Aheb. 11:6.
▪ Tisalole Chilichonse Kutisokoneza Potumikira Yehova
▪ Tiziganizira Kwambiri za Yehova
Masiku ano pali zinthu zambiri zimene zingatisokoneze potumikira Yehova. Koma kodi tingatani kuti zinthu zimenezi zisatisokoneze? Nanga tingatani kuti tizimvetsa komanso kukumbukira zimene timawerenga m’Mawu a Mulungu? Nkhani ziwirizi zikuyankha mafunso amenewa.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 Tizilemekeza Kwambiri Abale Ngati Amenewa
14 Sananong’oneze Bondo ndi Zimene Anasankha Ali Mnyamata
PATSAMBA LOYAMBA: M’bale akuchititsa msonkhano wokonzekera utumiki m’katauni kotchedwa St. Helens, ku Tasmania
TASMANIA, KU AUSTRALIA
KULI ANTHU
514,800
KULI MIPINGO
24
KULI OFALITSA
1,779
WOFALITSA ALIYENSE AYENERA KULALIKIRA ANTHU