Zamkatimu
November 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
DECEMBER 28, 2015–JANUARY 3, 2016
Muziphunzitsa Ana Anu Aang’ono Kuti Azitumikira Yehova
TSAMBA 3
JANUARY 4-10, 2016
Muziphunzitsa Ana Anu Achinyamata Kuti Azitumikira Yehova
TSAMBA 8
JANUARY 11-17, 2016
TSAMBA 16
JANUARY 18-24, 2016
Kodi ‘Mumakonda Anzanu Ngati Mmene Mumadzikondera Nokha’?
TSAMBA 21
JANUARY 25-31, 2016
Zimene Zachitika M’zaka 100 Zimene Ufumu Wakhala Ukulamulira
TSAMBA 26
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Muziphunzitsa Ana Anu Aang’ono Kuti Azitumikira Yehova
▪ Muziphunzitsa Ana Anu Achinyamata Kuti Azitumikira Yehova
Yehova anapatsa makolo udindo wofunika kwambiri wophunzitsa ana awo kuti azimutumikira. Nkhani ziwirizi zikufotokoza zimene makolo angachite kuti azitsanzira Yesu pophunzitsa ana awo mwachikondi, modzichepetsa ndiponso mozindikira.
▪ Yehova Ndi Mulungu Wachikondi
▪ Kodi ‘Mumakonda Anzanu Ngati Mmene Mumadzikondera Nokha’?
Nkhani yoyamba ikusonyeza kuti Yehova ndi Mulungu wachikondi. Ikufotokozanso zimene Mulungu wachita posonyeza kuti amakonda anthu. Nkhani yachiwiri ikufotokoza zimene atumiki a Yehova angachite posonyeza kuti amakonda anzawo.
▪ Zimene Zachitika M’zaka 100 Zimene Ufumu Wakhala Ukulamulira
Nkhaniyi ikufotokoza zimene anthu a Mulungu achita polalikira uthenga wabwino m’zaka 100 zimene Ufumu wakhala ukulamulira. Ikufotokozanso zinthu ndiponso njira zina zimene tagwiritsa ntchito polalikira. M’nkhaniyi tionanso maphunziro amene athandiza kuti abale ndi alongo azilalikira mwaluso.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
13 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
14 Tiziyamikira Zimene Yehova Amatipatsa
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Woyang’anira dera ndiponso apainiya apadera akwera boti kuti apite kumadera a m’nkhalango ya m’mphepete mwa mtsinje wa Amazon. Iwo amasangalala kulalikira uthenga wabwino m’midzi imene ili m’mbali mwa mtsinjewu
BRAZIL
KULI ANTHU
203,067,835
KULI OFALITSA
794,766
KULI APAINIYA
84,550
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO MU 2014