Zamkatimu
December 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
FEBRUARY 1-7, 2016
TSAMBA 4
FEBRUARY 8-14, 2016
Baibulo Lomveka Bwino Kwambiri
TSAMBA 9
FEBRUARY 15-21, 2016
Muzigwiritsa Ntchito Bwino Lilime Lanu
TSAMBA 18
FEBRUARY 22-28, 2016
Yehova Adzakuthandizani Pamene Mukudwala
TSAMBA 23
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Yehova Amalankhula Nafe
▪ Baibulo Lomveka Bwino Kwambiri
Kwa zaka zambiri, Yehova wakhala akulankhula ndi atumiki ake m’zilankhulo zosiyanasiyana. M’nkhanizi tikambirana mmene wachitira zimenezi. Tikambirananso mmene Baibulo la Dziko Latsopano lathandizira kuti anthu adziwe dzina la Mulungu ndiponso zimene iye amafuna.
▪ Muzigwiritsa Ntchito Bwino Lilime Lanu
Mulungu anatipatsa mphatso yamtengo wapatali ya kulankhula. M’nkhaniyi tikambirana zinthu zitatu zokhudza kulankhula. Tikambirananso kuti tiyenera kutsanzira Yesu pa nkhani yogwiritsa ntchito mphatsoyi potamanda Mulungu ndiponso kulimbikitsa ena.
▪ Yehova Adzakuthandizani Pamene Mukudwala
Popeza tonsefe timadwala, kodi tingayembekezere kuti Yehova atichiritse mozizwitsa ngati mmene ankachitira ndi anthu ena akale? Kodi tiyenera kuganizira mfundo ziti anthu ena akatipatsa malangizo okhudza mankhwala? Nkhaniyi itithandiza kupeza mayankho a mafunsowa ndiponso kuona mmene tingasankhire zinthu mwanzeru pa nkhani ya mankhwala.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
14 Baibulo la Dziko Latsopano Lokonzedwanso Lomwe Linatuluka mu 2013
PATSAMBA LOYAMBA: Mpainiya wapadera akulalikira mayi wina ndiponso ana ake. M’dzikoli anthu ambiri amalankhula Chisipanishi ndi Chiguwarani. Abale ndi alongo amalalikira m’zilankhulo ziwiri zonsezi
PARAGUAY
KULI ANTHU
6,800,236
KULI OFALITSA