Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
3 Kodi Utumiki Wanu Uli Ngati Mame?
MLUNGU WA MAY 30, 2016–JUNE 5, 2016
5 Yehova Amadalitsa Anthu Okhulupirika
Nkhaniyi ikufotokoza zimene Yefita ndi mwana wake wamkazi anachita kuti apitirize kutsatira mfundo za Yehova ngakhale kuti ankakumana ndi mavuto. Tiphunziranso kuti kukhala okhulupirika kwa Mulungu n’kofunika kwambiri kuposa chilichonse.
10 Luso Loona Zinthu M’maganizo Mwathu
MLUNGU WA JUNE 6-12, 2016
13 “Mulole Kuti Kupirira Kumalize Kugwira Ntchito Yake”
Tiyenera kupirira mpaka mapeto kuti tidzalandire moyo wosatha. Nkhaniyi ikufotokoza zinthu 4 zimene zingatithandize kupirira komanso zitsanzo za anthu atatu amene anakhalabe okhulupirika pamene ankakumana ndi mavuto. Ikufotokozanso mmene kupirira kungamalizire ntchito yake kwa Mkhristu aliyense.
MLUNGU WA JUNE 13-19, 2016
18 N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonkhana?
Akhristufe timakumana ndi mavuto amene angatilepheretse kusonkhana. Nkhaniyi ikufotokoza zimene tingachite kuti tizifikabe pamisonkhano nthawi zonse. Tionanso mmene misonkhano ingatithandizire ifeyo ndi anthu ena komanso mmene Yehova amamvera tikamasonkhana.
23 Mbiri ya Moyo Wanga—Masisitere Anasintha N’kukhala Alongo
MLUNGU WA JUNE 20-26, 2016
Popeza kuti maboma a dzikoli awonongedwa posachedwapa, akhoza kuyamba kutikakamiza kuti tilowerere ndale. Nkhaniyi ikufotokoza zinthu 4 zimene zingatithandize kukhalabe okhulupirika.