Magazini Yophunzira
April 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: MAY 30 MPAKA JUNE 26, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
COLOMBIA
Anthu Achiwayu amakonda Mulungu. Abale ndi alongo amayesetsa kuwathandiza kuti amve uthenga wabwino. Anthuwa ali ndi luso loluka zinthu pamanja ndipo amakazigulitsa mumzinda wina wa m’dzikoli. Kumeneko abale amawalalikira uthenga wabwino.
KULI OFALITSA
166,049
MAPHUNZIRO A BAIBULO
229,723
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
510,952
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.