Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
3 Anadzipereka ndi Mtima Wonse—Ku Ghana
MLUNGU WA AUGUST 29, 2016–SEPTEMBER 4, 2016
7 Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina
Yesu anatiphunzitsa kuti ‘tizifunafuna Ufumu choyamba,’ osati zinthu zina. Kodi tingatani kuti tipewe msampha wokonda chuma komanso kuti tikhale ndi moyo wosalira zambiri n’cholinga choti tiziika zinthu za Ufumu pamalo oyamba? M’nkhaniyi tikambirana mawu a Yesu opezeka pa Mateyu 6:25-34 omwe ananena pa ulaliki wake wapaphiri.
MLUNGU WA SEPTEMBER 5-11, 2016
13 N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kukhalabe Maso’?
Masiku otsiriza ano, m’pofunika kwambiri kumvera malangizo a Yesu akuti ‘tikhalebe maso.’ (Mat. 24:42) Kuti zimenezi zitheke, tiyenera kupewa zinthu zimene zingatilepheretse kukhala maso. Nkhaniyi ikufotokoza mmene tingachitire zimenezi.
18 “Usachite Mantha. Ineyo Ndikuthandiza”
MLUNGU WA SEPTEMBER 12-18, 2016
21 Tiziyamikira Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu
MLUNGU WA SEPTEMBER 19-25, 2016
26 Tizilalikira Uthenga wa Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu
Nkhani ziwirizi zikufotokoza mmene kukoma mtima kwakukulu kwa Yehova kumatithandizira. Zikufotokozanso mmene tingasonyezere kuyamikira pothandiza ena kuti nawonso apindule ndi khalidwe la Yehova limeneli.