Magazini Yophunzira
JULY 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: AUGUST 29 MPAKA SEPTEMBER 25, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
DOMINICAN REPUBLIC
Mpainiya wapadera akulalikira m’mbali mwa nyanja ku Las Terrenas kwa munthu amene wakolola kokonati
KULI OFALITSA
37,536
MAPHUNZIRO A BAIBULO
69,892
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
120,103
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.