Magazini Yophunzira
APRIL 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: MAY 29 MPAKA JULY 2, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
ZAMBIA
Kagulu ka ofalitsa kamumzinda wa Lusaka ku Zambia kakonzekera utumiki pa Nyumba ya Ufumu ndipo kakupita kukalalikira. Nyumba ya Ufumu yosamaliridwa bwinoyi imathandiza kuti anthu ayambe kuphunzira za Yehova.
KULI OFALITSA
183,586
MAPHUNZIRO A BAIBULO
415,706
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
782,527
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.