Magazini Yophunzira
MAY 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JULY 3-30, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
ECUADOR
Mpainiya wokhazikika akulalikira m’chilankhulo cha Chikichuwa kwa munthu amene akugulitsa zinthu mumsika wamumzinda wa Otavalo, chakumpoto kwa dziko la Ecuador.
KULI OFALITSA
90,110
MAPHUNZIRO A BAIBULO
148,637
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
274,593
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.