Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
MLUNGU WA JULY 3-9, 2017
3 Tizithandiza Alendo Kuti ‘Azitumikira Yehova Mokondwera’
MLUNGU WA JULY 10-16, 2017
8 Kodi Tingathandize Bwanji Ana a Anthu Ochokera M’mayiko Ena?
Nkhani yoyamba ikufotokoza mavuto amene abale ndi alongo omwe athawa kwawo amakumana nawo komanso zimene tingachite powathandiza. Nkhani yachiwiri ikufotokoza mmene mfundo za m’Baibulo zingathandizire anthu amene asamukira m’dziko lina kuti azisankha zinthu mwanzeru pothandiza ana awo.
13 Mbiri ya Moyo Wanga—Vuto Losamva Silinandilepheretse Kuphunzitsa Anthu Ena Baibulo
MLUNGU WA JULY 17-23, 2017
17 Musalole Kuti Chikondi Chanu Chizirale
MLUNGU WA JULY 24-30, 2017
22 “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?”
Kukhala m’dziko loipali si kophweka. Koma nkhanizi zikusonyeza mmene tingapewere mtima wodzikonda wa m’dzikoli tikamapitiriza kukonda Yehova, choonadi ndiponso abale ndi alongo athu. Zikufotokozanso zimene tingachite kuti tizikonda kwambiri Khristu m’malo mokonda zinthu za m’dzikoli.
27 Kodi Gayo Ankathandiza Bwanji Akhristu Anzake?
30 Moyo Wosalira Zambiri Ndi Wosangalatsa
31 Kale Lathu