Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w17 June tsamba 2
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
w17 June tsamba 2

Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

3 Kodi Mukukumbukira?

MLUNGU WA JULY 31, 2017–AUGUST 6, 2017

4 Yehova Amatitonthoza M’masautso Athu Onse

Tonsefe timakumana ndi mavuto koma Yehova amatilimbikitsa. Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zimene Yehova watipatsa zomwe zingatilimbikitse panopa komanso m’tsogolo.

MLUNGU WA AUGUST 7-13, 2017

9 Tizikonda ndi Mtima Wonse Chuma Chimene Mulungu Watipatsa

Nkhaniyi ikufotokoza zimene tingachite potsatira mfundo zimene tikuphunzira mufanizo la Yesu la wamalonda amene ankafunafuna ngale. Itithandizanso kudzifufuza pa nkhani ya mmene timaonera utumiki wathu ndiponso mfundo za m’Baibulo zimene taphunzira.

14 Tisamaweruze Anthu Chifukwa cha Maonekedwe Awo

16 Kodi Mumathetsa Kusamvana N’kukhazikitsa Mtendere?

21 “Udalitsike Chifukwa cha Kulingalira Bwino Kwako”

MLUNGU WA AUGUST 14-20, 2017

22 Musamaiwale Nkhani Yofunika Kwambiri

MLUNGU WA AUGUST 21-27, 2017

27 Muzikhala Kumbali ya Ulamuliro wa Yehova

Chifukwa chotanganidwa ndi zinthu za tsiku ndi tsiku tikhoza kuiwala zinthu zofunika. Nkhanizi zitithandiza kuzindikira kuti nkhani ya ulamuliro wa Yehova ndi yofunika kwambiri. Zitithandizanso kudziwa mmene tingasonyezere kuti tili kumbali ya ulamulirowo

32 Kodi Mukudziwa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena