Magazini Yophunzira
JUNE 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JULY 31–AUGUST 27, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
GREECE
Mabanja a ku Athens akuphunzira nyimbo za Ufumu
KULI OFALITSA
28,816
MAPHUNZIRO A BAIBULO
13,237
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
46,822
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.