Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
3 Mbiri ya Moyo Wanga—Timadalitsidwa Tikamachita Zimene Yehova Amatiuza
MLUNGU WA NOVEMBER 27, 2017–DECEMBER 3, 2017
7 “Tizisonyezana Chikondi Chenicheni M’zochita Zathu”
Akhristu oona amadziwika ndi nkhani yosonyezana chikondi chenicheni. Nkhaniyi ikufotokoza njira 9 zimene tingasonyezere “chikondi chopanda chinyengo.”—2 Akor. 6:6.
MLUNGU WA DECEMBER 4-10, 2017
12 Choonadi Sichibweretsa “Mtendere Koma Lupanga”
Anthu a Yehova amavutika akamatsutsidwa ndi achibale awo omwe si Mboni. Munkhaniyi tiphunzira zimene zingatithandize tikakumana ndi vuto limeneli.
17 Yosefe wa ku Arimateya Analimba Mtima
MLUNGU WA DECEMBER 11-17, 2017
21 Kodi Masomphenya a Zekariya Akukukhudzani Bwanji?
MLUNGU WA DECEMBER 18-24, 2017
26 Timatetezedwa ndi Magaleta Komanso Chisoti Chachifumu
Nkhanizi zikufotokoza masomphenya a nambala 6, 7 ndi 8 amene Zekariya anaona. Masomphenya a nambala 6 ndi 7 atithandiza kuona kuti ndi mwayi waukulu kukhala m’gulu loyera la Mulungu. Masomphenya a nambala 8 akusonyeza mmene Yehova amatitetezera n’cholinga choti tizimulambira moyenera.