Magazini Yophunzira
OCTOBER 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: NOVEMBER 27–DECEMBER 24, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
NIGERIA
Akulalikira pamalo ena amene amaika mashelefu mumzinda wa Lagos, womwe uli ndi anthu ambiri kuposa mizinda yonse ya mu Africa. Pamalowa, mwezi uliwonse anthu pafupifupi 6 amapempha kuti aziphunzira Baibulo
KULI OFALITSA
370,336
MAPHUNZIRO A BAIBULO
870,185
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
774,874
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.