Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw Library Komanso Jw.Org
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Manja a Octopus Ndi Ogometsa Kwambiri
Akatswiri apanga makina ogwira ntchito ngati manja potengera manja odabwitsa a octopus n’cholinga choti azithandiza madokotala pochita opaleshoni.
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > WAS IT DESIGNED?
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
“Ndinkadzikumbira Ndekha Manda”
Óscar anali chigawenga ku El Salvador ndipo amaona kuti akanapanda kuthandizidwa ndi Mawu a Mulungu sakanakhalabe ndi moyo. Kodi n’chiyani chinamuthandiza kuti asinthe?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > BIBLE CHANGES LIVES.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDERE KOMANSO MOYO WOSANGALALA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.