Magazini Yophunzira
AUGUST 2019
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: SEPTEMBER 30–OCTOBER 27, 2019
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
PATSAMBA LOYAMBA:
Paulo ali pa ukaidi wosachoka panyumba ku Roma, analembera mpingo wa ku Filipi kalata ndipo ankalalikira anthu omulondera komanso ena amene anabwera kudzamuona. (Onani nkhani yophunzira 32, ndime 16)