Mbiri Yateokratiki
Haiti: May unali mwezi wapadera ndi chiŵerengero chapamwamba chatsopano cha ofalitsa 9,188, kuwonjezeka kwa 13 peresenti kuposa avareji ya chaka chatha.
Italy: Kunali chiŵerengero chapamwamba chatsopano cha ofalitsa 205,128 m’May. Chimenechi chinaposa chiŵerengero chapamwamba cha ofalitsa cha m’mwezi umodzi wapita ndi 1,499.