Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 3/96 tsamba 5
  • Zilengezo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zilengezo
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—1996
Utumiki Wathu wa Ufumu—1996
km 3/96 tsamba 5

Zilengezo

◼ Mabuku ogaŵira mu March: Knowledge That Leads to Everlasting Life. Mipingo imene ilibe buku la Knowledge mu sitoko ingagwiritsire ntchito buku la Kukhala ndi Moyo Kosatha. April ndi May: Sabusikripishoni ya Nsanja ya Olonda. June: Knowledge That Leads to Everlasting Life.

◼ Woyang’anira wotsogoza kapena winawake woikidwa ndi iye ayenera kuŵerengera maakaunti a mpingo pa March 1 kapena mwamsanga pambuyo pake. Lengezani ku mpingo mutachita zimenezi.

◼ Monga momwe tinalengezera m’kope lathu la Utumiki Wathu Waufumu la January 1996, nkhani yapoyera yapadera ya nyengo ya Chikumbutso chaka chino idzaperekedwa m’mipingo yochuluka pa Sande, April 21. Nkhaniyo ili ndi mutu wakuti “Kukhala Opanda Banga Pakati pa Mbadwo Wokhotakhota.” Muyenera kupanga kuyesayesa kwapadera kuti muitane aja amene adzafika pa Chikumbutso pa April 2.

◼ Kuyambira pa June 3, 1996 tidzaphunzira buku la Knowledge That Leads to Everlasting Life pa Phunziro la Buku la Mpingo.

◼ Zofalitsa Zomwe Zilipo:

1996 Yearbook of Jehovah’s Witnesses.—Chingelezi

Mabaundi voliyumu a 1960-1994 a Watchtower.—Chingelezi

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena