Zilengezo
◼ Mabuku ogaŵira mu June: Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha. Sumikani maganizo pakuyambitsa maphunziro a Baibulo apanyumba. July ndi August: Lililonse la mabrosha a masamba 32 otsatirawa: Boma Limene Lidzabweretsa Paradaiso, Kodi Chifuno cha Moyo Nchiyani—Kodi Mungachipeze Motani?, Kodi Mulungu Amatisamaliradi?, Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu?, Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira ndi Sangalalani ndi Moyo Padziko Lapansi Kosatha! September: Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja.
◼ Woyang’anira wotsogoza kapena wina amene iye wamsankha aŵerengere maakaunti a mpingo pa June 1 kapena mwamsanga pambuyo pake. Mutachita zimenezo, lengezani ku mpingo.
◼ Madiski a Nyimbo Omwe Alipo:
Kingdom Melodies 2, 3 (Chonde onani kuti ameneŵa si makaseti iyayi koma madiski ofuna wailesi yapadera. Madiskiwo ali ndi nyimbo zofanana ndi zimene zili pakaseti ndi nambala yomwe).
Singing Kingdom Songs—Chingelezi
◼ Vidiyokaseti Yatsopano Imene Ilipo:
Jehovah’s Witnesses Stand Firm Against Nazi Assault—Chingelezi