Lipoti Lautumiki la April
Av. Av. Av. Av.
Chiŵerengero cha: Maola Mag. M.O. Maph.
Apai. Apad. 4 140.3 25.8 94.8 7.0
Apainiya 2,539 88.9 3.0 32.5 3.0
Apai. Otha. 3,999 56.8 1.5 19.7 1.9
Ofalitsa 34,200 11.0 0.2 4.2 0.5
PAMODZI 40,742a Obatizidwa: 504
[Mawu a M’munsi]
a Kachiŵirinso chimenechi ndicho chiŵerengero chapamwamba chatsopano chimene chikusonyeza kuwonjezeka kwa 14 peresenti kuposa chaka chatha chautumiki. Ndithudi Yehova akudalitsa ntchito imene mipingo ikuchita. Tikukuthokozani abale ndi alongo!