Phunziro la Buku la Mpingo
Ndandanda ya maphunziro a mpingo m’brosha lakuti: Kodi Mwazi Ungapulumutse Motani Moyo Wanu?
June 1: Mlungu Wachisanu
Ndandanda ya maphunziro a mpingo m’buku la Ogwirizana m’Kulambiridwa kwa Mulungu Yekha Wowona
June 8: Masamba 5 mpaka 9, (4)
June 15: Masamba 9, (5) mpaka 14, ndime 5
June 22: Masamba 14, ndime 6 mpaka 17, (4)
June 29: Masamba 18, (5) mpaka 22, ndime 6
Manambala amene ali m’mabulaketi ndi a mafunso amene ali m’ndime.