Samalani Ulosi wa Danieli!
Ndandanda yophunzirira kuyambira mlungu wa June 27, 2005, mpaka mlungu wa April 10, 2006
MLUNGU WA MUTU NDIME MAVESI OPHUNZIRA
June 27 1 1-18
July 4 2 1-15
11 2 16-32
18 3 1-14 Dan. 1:1-7
25 3 15-26 Dan. 1:8-15
Aug. 1 3 27-37 Dan. 1:16-21
8 4 1-11 Dan. 2:1-39
15 4 12-24* Dan. 2:39, 40
22 4 25-36 Dan. 2:41-49
29 5 1-17 Dan. 3:1-18
Sept. 5 5 18-25* Dan. 3:19-30
12 6 1-14 Dan. 4:1-27
19 6 15-29 Dan. 4:28-37
26 7 1-16 Dan. 5:1-23
Oct. 3 7 17-28 Dan. 5:24-31
10 8 1-16 Dan. 6:1-17
17 8 17-29 Dan. 6:18-28
24 9 1-12 Dan. 7:1-5
31 9 13-19 Dan. 7:6, 7
Nov. 7 9 20-32 Dan. 7:8
14 9 33-40 Dan. 7:9-28
21 10 1-15 Dan. 8:1-8
28 10 16-30 Dan. 8:9-27
Dec. 5 11 1-12 Dan. 9:1-23
12 11 13-20 Dan. 9:24, 25
19 11 21-30 Dan. 9:26, 27
26 12 1-13 Dan. 10:1-8
Jan. 2 12 14-22 Dan. 10:9-21
9 13 1-15 Dan. 11:1-4
16 13 16-30 Dan. 11:5-16
23 13 31-9 Dan. 11:17-19
30 14 1-15 Dan. 11:20-24
Feb. 6 14 16-27 Dan. 11:25, 26
13 15 1-15 Dan. 11:27-30a
20 15 16-25 Dan. 11:30b, 31
27 16 1-17 Dan. 11:32-41
Mar. 6 16 18-28 Dan. 11:42-45
13 17 1-12 Dan. 12:1-3
20 17 13-23 Dan. 12:4-11
27 17 24-9 Dan. 12:12
Apr. 3 18 1-12 Dan. 12:13
10 18 13-27 Dan. 12:13
Werengani ndi kukambirana nkhani zowonjezera pamene mukuphunzira ndime kapena funso pamene asonyeza kuti muchite zimenezi. Mwachitsanzo, bokosi lakuti “Mfundo ya Chinenero” (tsa. 26 m’buku la zilembo za nthawi zonse, ndipo tsa. 32 ndi 33 m’buku la zilembo zazikulu) liyenera kuphunziridwa limodzi ndi mutu 2, ndime 25, funso (c). Kambiranani matchati ndi zithunzi za m’bukuli pa malo amene zikugwirizana ndi phunziro. Chonde dziwani kuti buku la zilembo zazikulu lilibe zithunzi kapena matchati amene ali patsamba 56, 139, 188 ndi 189 m’buku la zilembo za nthawi zonse. Pamapeto pa phunziro la mlungu uliwonse, werengani ndi kukambirana “mavesi ophunzira” m’buku la Danieli m’Baibulo, ngati nthawi ilipo.
* Bwerezaninso kukambirana “mavesi ophunzira” a mlungu watha, ngati nthawi ilipo.