Ndandanda ya Mlungu wa April 27
MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 27
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 18 ndime 7-15.
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Eksodo 19-22
Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.8: Fotokozani mwachidule Bokosi la Mafunso.
Mph.12: “Msonkhano Wachigawo wa Mboni za Yehova wa 2009.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho. Ikambidwe ndi mlembi wa mpingo. Tsindikani kufunika kosonyeza chipatso cha mzimu nthawi zonse.—Agal. 5:22, 23.
Mph.10: “Kodi Nyumba ya Ufumu Yanu Mumaiona Bwanji?”