Ndandanda ya Mlungu wa November 16
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 16
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 29 ndime 13-21, ndi bokosi patsamba 299
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Deuteronomo 23-27
Na. 1: Deuteronomo 25:1-16
Na. 2: Ana Amene Amakondweretsa Mulungu (lr-CN mutu 41)
Na. 3: Kodi Ndi Zinthu Ziti Zimene Tiyenera Kuziona Kukhala Zopatulika?
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Khalani Wozindikira Ndipo Afikeni Pamtima Anthu. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 258, ndime 1, mpaka tsamba 259, ndime 3.
Mph. 10: Tsogolerani Anthu Achidwi ku Gulu la Yehova. Nkhani yokambirana ndi omvera kuchokera m’buku la Gulu, patsamba 99, ndime 2, mpaka patsamba 100, ndime 1. Chitaninso chitsanzo chachidule chosonyeza mfundo imodzi pa mfundo zimene zafotokozedwa m’nkhaniyi.
Mph. 10: “Yakani ndi Mzimu.” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.