Zilengezo
◼ January: Gawirani buku la Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? February: Gawirani mabuku awa ngati alipo: Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? kapena Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja. March: Gawirani buku la Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Ofalitsa ayenera kukhala ndi cholinga choyambitsa maphunziro a Baibulo akagawira bukulo kapena akapeza mwininyumba amene ali nalo kale.
◼ Kuyambira mu February, nkhani ya onse ya oyang’anira madera idzakhala ya mutu wakuti “Zimene Ufumu wa Mulungu Ukutichitira Masiku Ano.”