Ndandanda ya Mlungu wa February 1
MLUNGU WOYAMBIRA FEBRUARY 1
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
lv mutu 3, ndime 1-7 ndi bokosi patsamba 29
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Oweruza 8-10
Na. 1: Oweruza 8:1-12
Na. 2: Kodi Pali Chilango Chamuyaya Kaamba ka Oipa? (rs tsa. 146 ndime 3 mpaka tsa. 147 ndime 2)
Na. 3: Kodi Kudziwa Zimene Zimachitika Munthu Akamwalira N’kothandiza Bwanji?
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Zosowa za Pampingo.
Mph. 10: Kuyambitsa Maphunziro a Baibulo. Tchulani tsiku loyambitsa maphunziro a Baibulo. Tchulani zinthu zosangalatsa zimene zinachitika mu utumiki wakumunda. Apo ayi funsani woyang’anira utumiki kapena wofalitsa waluso kuti afotokoze njira yoyambitsira maphunziro a Baibulo yothandiza kwambiri m’dera lanu. Mwina mungamupemphe kuti achite chitsanzo cha zimene zinachitika.
Mph. 10: Gwiritsani Ntchito Zinthu Zooneka mu Utumiki. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki patsamba 247 ndime 1 mpaka 248 ndime 1.