Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu June: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena buku lina lililonse limene linasindikizidwa chisanafike chaka cha 1995. July ndi August: Ofalitsa angagawire kalikonse mwa timabuku tamasamba 32 timene ali nato monga: Dikirani!, Kodi Mulungu Amatisamaliradi?, Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu?, Sangalalani ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha!, ndi “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano.” September: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Yesetsani kuyambitsa maphunziro a Baibulo pa ulendo woyamba.