Ndandanda ya Mlungu wa July 5
MLUNGU WOYAMBIRA JULY 5
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
lv mutu 9 ndime 1-12 ndi bokosi patsamba 101a
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Mafumu 7-8
Na. 1: 1 Mafumu 8:14-26
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Timachenjezedwa Kuti Sitiyenera Kudziona Ngati Anzeru? (Yes. 5:21)
Na. 3: Kodi Anthu Amapezadi Ufulu Akanyalanyaza Mfundo za M’Baibulo Zokhudza Kugonana? (rs tsa. 171 ndime 1-3)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Njira Zowonjezera Utumiki Wanu—Gawo 1. Nkhani yochokera m’buku la Gulu, tsamba 111, ndime 1 mpaka tsamba 112, ndime 2. Funsani wofalitsa mmodzi kapena awiri amene asamukira kudera lina kapena kuphunzira chinenero china n’cholinga chowonjezera utumiki wawo. Kodi amakumana ndi mavuto otani? Kodi banja lawo kapena mpingo unawathandiza bwanji? Kodi apeza madalitso otani?
Mph. 10: Thandizani Ophunzira Anu Kudzifufuza. Nkhani yokambirana ndi omvera kuchokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 261 ndime 1 mpaka kumapeto kwa tsamba 262.
[Mawu a M’munsi]
a Mungasankhe kukambirana bokosi kapena ayi.