Ndandanda ya Mlungu wa July 12
MLUNGU WOYAMBIRA JULY 12
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
lv mutu 9, ndime 13-21 ndi bokosi patsamba 104
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Mafumu 9-11
Na. 1: 1 Mafumu 9:10-23
Na. 2: Kodi Baibulo Limanena Chiyani pa Nkhani Yofunafuna Chuma ndi Kumwa Kwambiri Zoledzeretsa? (rs tsa. 171 ndime 4 ndi 5)
Na. 3: Mmene Akhristu Enieni Amasonyezera Nzeru Yochokera Kumwamba (Yak. 3:17)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph . 20: “Misonkhano Yachigawo Ndi Nthawi Imene Timalambira Mulungu Mosangalala.” Nkhani yokambirana mwa mafunso ndi mayankho. Ngati nthawi ilipo kambirananinso mfundo zazikulu m’nkhani yakuti “Zofunika Kukumbukira pa Msonkhano Wachigawo,” imene ili patsamba 6.
Mph . 10: “Ntchito Yathu Yaikulu.” Nkhani yokambirana mwa mafunso ndi mayankho.