Ndandanda ya Mlungu wa November 8
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 8
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
lv mutu 14 ndime 15-19, ndi bokosi la patsamba 167
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Mbiri 21-25
Na. 1: 1 Mbiri 22:11-19
Na. 2: Kodi Tingatani Kuti Tipitirize Kukonda Kwambiri Choonadi?
Na. 3: Kodi Mboni za Yehova Zimadziwa Bwanji Mfundo za M’Baibulo Zimene Zimaphunzitsa? (rs tsa. 276 ndime 1-4)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Kodi Mumaopa Akufa? Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera mu Nsanja ya Olonda ya January 1, 2009, tsamba 11 mpaka 13. Pemphani omvera kuti afotokoze ubwino wodziwa zoona zenizeni zokhudza akufa.
Mph. 15: “M’minda Mwayera Kale Ndipo M’mofunika Kukolola.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.