Ndandanda ya Mlungu wa March 14
MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 14
Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 4 ndime 1-10 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yobu 1-5 (Mph. 10)
Na. 1: Yobu 3:1-26 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Tingaphunzire Chiyani pa Chitsanzo cha Ana Aakazi a Tselofekadi?—Num. 36:10-12 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Zozizwitsa Zimene Yesu Anachita Zimatsimikizira Kuti Iye Ndi Mulungu?—rs tsa. 429 ndime 4–tsa. 430 ndime 2 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Kutumikira Yehova Kumatilemeretsa. (Miy. 10:22) Nkhani yokambirana. Pemphani omvera kuti anene mmene akuyamikirira chuma chenicheni chimene chimapezeka potumikira Yehova.
Mph. 15: “Tiyeni Tisonyeze Kuyamikira.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho. Fotokozani zimene mpingo wakonza pokonzekera Chikumbutso.
Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero