Zilengezo
◼ Mabuku ogawira m’mwezi wa March: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Yesetsani kuyambitsa maphunziro a Baibulo. April ndi May: Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! Mukamachita maulendo obwereza kwa anthu achidwi komanso amene anabwera ku Chikumbutso kapena pa zochitika zina zauzimu, muziyesetsa kuyambitsa maphunziro ndi buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani. June: Gawirani buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?