Ndandanda ya Mlungu wa April 11
MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 11
Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 5 ndime 9-15 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yobu 21-27 (Mph. 10)
Na. 1: Yobu 25:1–26:14 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Mtanda Suyenera Kugwiritsidwa Ntchito Polambira? (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Yesu Khristu Ndi Mikayeli Mkulu wa Angelo Ndi Munthu Mmodzi?—rs tsa. 432 ndime 1-3 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo. Uzani mpingo mmene ntchito yoitanira anthu ku Chikumbutso ikuyendera pa mpingo wanu.
Mph. 15: Mmene Tingalalikirire Pogwiritsa Ntchito Kalata. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 71-73.
Mph. 15: “Umboni Wamphamvu Udzaperekedwa.” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero