Ndandanda ya Mlungu wa November 7
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 7
Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 15 ndime 8-16 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Miyambo 27-31 (Mph. 10)
Na. 1: Miyambo 28:19–29:10 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Lemba la Aroma 8:32 Limatitsimikizira Motani Kuti Malonjezo Onse a Mulungu Adzakwaniritsidwa? (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Lemba la Luka 21:11 Lakhala Likukwaniritsidwa Motani Kuyambira mu 1914?—rs tsa. 263 ndime 2 mpaka tsa. 264 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Kuyankha Mafunso Okhudza Kuthiridwa Magazi. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Kukambitsirana, tsamba 317, ndime 1 mpaka tsamba 319, ndime 1. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mpainiya ali mu utumiki wa nyumba ndi nyumba ndipo akuyankha funso limodzi mwa mafunso opezeka pa ndimezi. Poyankha funsolo iye agwiritse ntchito buku la Kukambitsirana.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Njira Zowonjezera Utumiki Wanu. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Gulu, tsamba 110, ndime 1 mpaka tsamba 114 ndime 3.
Nyimbo Na. 15 ndi Pemphero