Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 3/12 tsamba 8
  • Zilengezo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zilengezo
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
km 3/12 tsamba 8

Zilengezo

◼ Mabuku ogawira m’mwezi wa March: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Yesetsani kuyambitsa maphunziro a Baibulo pa ulendo woyamba. April ndi May: Gawirani magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! Mukapeza anthu achidwi, agawireni kapepala kakuti, Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi? Popanga maulendo obwereza kwa anthu amene anabwera pa Chikumbutso kapena pa misonkhano ina koma safika pa misonkhano ya mpingo nthawi zonse, yesetsani kuyambitsa maphunziro a Baibulo pogwiritsa ntchito buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani. June: Gawirani buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? ndipo muyesetse kuyambitsa phunziro la Baibulo pa ulendo woyamba.

◼ Chaka chino Chikumbutso chidzachitika Lachinayi pa April 5, 2012. Ngati mpingo wanu umachita misonkhano Lachinayi, muyenera kusinthira tsiku lina mkati mwa mlunguwo ngati mipingo ina siigwiritsa ntchito Nyumba ya Ufumuyo. Ngati n’zosatheka kuti musunthire misonkhanoyo tsiku lina, mungadzaphatikize nkhani zimene ndi zothandiza kwambiri kwa mpingo wanu pa Msonkhano wa Utumiki wina.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena