Ndandanda ya Mlungu wa May 7
MLUNGU WOYAMBIRA MAY 7
Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 5 ndime 17 mpaka 22 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yeremiya 35-38 (Mph. 10)
Na. 1: Yeremiya 36:14-26 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Mariya Anakhala Namwali Moyo Wake Wonse?—rs tsa. 255 ndime 5 mpaka tsa. 256 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Zochita Zathu Zingasangalatse Kapena Kukwiyitsa Yehova?—Ower. 2:11-18 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 20: Kodi Mwayesapo? Nkhani yokambirana. Fotokozani mfundo za mu nkhani zotsatirazi zimene zinatuluka mu Utumiki Wathu wa Ufumu posachedwapa: “Musalephere Kulalikira” (km 10/11), “Muziponya Nkhonya Zanu Mwanzeru” ndi yakuti, “Muzilalikira Anthu Amene Amalankhula Chinenero China” (km 1/12). Kenako funsani omvera kuti afotokoze mmene agwiritsira ntchito mfundo zopezeka m’nkhanizi ndiponso zimene apindula.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero