Ndandanda ya Mlungu wa June 4
MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 4
Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 7 ndime 1-8 ndi bokosi patsamba 53 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yeremiya 51-52 (Mph. 10)
Na. 1: Yeremiya 52:17-27 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi N’zoyenera Kupempha Mariya Kuti Akatiperekere Mapemphero Athu kwa Mulungu?—rs tsa. 258 ndime 4 mpaka tsa. 259 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Anthu Angalowe Bwanji “M’malo Otetezeka” a Yehova?—Sal. 91:1, 2, 9 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Mmene Tingawafikire Pamtima—Gawo 2. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 261, kuyambira ndime 1 mpaka kumapeto kwa tsamba 262.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Zimene Munganene Pogawira Magazini M’mwezi wa June. Nkhani yokambirana. Kwa mphindi imodzi kapena ziwiri, fotokozani nkhani zochepa zimene zili m’magaziniwo zimene zingakhale zothandiza m’gawo lanu. Kenako, pogwiritsa ntchito nkhani zoyambirira za mu Nsanja ya Olonda, pemphani omvera kuti anene funso lochititsa chidwi ndiponso lemba limene angawerenge pogawira magaziniwo. Chitaninso chimodzimodzi ndi nkhani zoyambirira m’magazini ya Galamukani! Ngati nthawi ilipo mungachitenso zimenezi ndi nkhani imodzi m’magazini ya Nsanja ya Olonda kapena Galamukani! Chitani chitsanzo chosonyeza mmene mungagawirire magazini iliyonse.
Nyimbo Na. 61 ndi Pemphero