Ndandanda ya Mlungu wa March 18
MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 18
Nyimbo Na. 120 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 20 ndime 8-15 ndi bokosi patsamba 161 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Luka 1-3 (Mph. 10)
Na. 1: Luka 1:24-45 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Ndani ali Oyenera Kudya Mkate Ndi Vinyo pa Mgonero wa Ambuye?—rs tsa. 72 ndime 3-4 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu Uyenera Kuchitika Liti Ndiponso Kangati?—rs tsa. 73 ndime 2-tsa. 74 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 12: “Alandireni Bwino.” Mafunso ndi mayankho. Chitani chitsanzo cha mbali ziwiri chosonyeza wofalitsa akulandira mlendo pa Chikumbutso. Kenako Chikumbutso chitatha, wofalitsayo akucheza ndi mlendoyo kuti apitirizebe kukhala ndi chidwi.
Mph. 18: “Mmene Mungagwiritsire Ntchito Kabuku Kakuti, Kodi Ndani Akuchita Chifuniro cha Yehova Masiku Ano?” Mafunso ndi mayankho. Chitani chitsanzo cha mphindi 7 chimene wofalitsa akukambirana ndi wophunzira Baibulo phunziro limodzi la m’kabukuka.
Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero