Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 4/13 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa May 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa May 6
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA MAY 6
Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
km 4/13 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa May 6

MLUNGU WOYAMBIRA MAY 6

Nyimbo Na. 26 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

bt mutu 22 ndime 15-21 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Yohane 1-4 (Mph. 10)

Na. 1: Yohane 3:22-36 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi “Kuyenda mwa Mzimu” Kumatanthauza Chiyani?—Agal. 5:16 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Imfa ya Yesu Khristu Imasiyana Bwanji Ndi Imfa ya Anthu Ena Amene Anaphedwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo?—rs tsa. 122 ndime 1-4 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 57

Mph. 10: Zimene Munganene Pogawira Magazini mu May. Nkhani yokambirana. Kwa masekondi 30 mpaka 60, fotokozani chifukwa chake magaziniwo angakhale othandiza m’gawo lanu. Kenako, pogwiritsa ntchito nkhani zoyambirira za mu Nsanja ya Olonda, pemphani omvera kuti anene funso lochititsa chidwi ndiponso lemba limene angawerenge pogawira magaziniwo. Chitaninso chimodzimodzi ndi nkhani zoyambirira m’magazini ya Galamukani! Ngati nthawi ilipo mungachitenso zimenezi ndi nkhani ina imodzi m’magazini ya Nsanja ya Olonda kapena Galamukani! Chitani chitsanzo chosonyeza mmene mungagawirire magazini iliyonse.

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Mph. 10: “Yehova Akapanda Kumanga Nyumba, Omanga Nyumbayo Amagwira Ntchito Pachabe” (Sal. 127:1) Nkhani yokambirana yochokera m’Buku Lapachaka la 2013, tsamba 149 ndime 1 mpaka tsamba 151 ndime 1. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene aphunzira pa ndime zimenezi.

Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena