Ndandanda ya Mlungu wa November 18
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 18
Nyimbo Na. 104 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 3 ndime 13 mpaka 19 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Aheberi 9-13 (Mph. 10)
Na. 1: Aheberi 10:19-39 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Kukhala pa Ubwenzi Ndi Mulungu N’Kofunikadi?—rs tsa. 88 ndime 4-5 (Mph. 5)
Na. 3: Njira Zimene Tingalimbikitsire Ena—Aroma 15:4; 2 Akor. 1:3, 4 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 10: Bokosi la Mafunso. Nkhani yokambirana. Kenako dziwitsani abale ndi alongo mmene ntchito yogawira Uthenga wa Ufumu Na. 38 ikuyendera pa mpingo wanu.
Mph. 10: “Tabwera Kuti . . . ” Nkhani yokambirana. Kenako, tchulani mabuku ogawira m’mwezi wa December, ndipo chitani chitsanzo chimodzi pogwiritsa ntchito mfundo za m’nkhaniyi. Kambirananinso zimene tikuphunzira pa nkhani yakuti Zochitika mu Utumiki Wakumunda patsamba 4.
Mph. 10: Yehova Amamva Mapemphero a Atumiki Ake. (1 Yohane 3:22) Nkhani yochokera mu Buku Lapachaka la 2013, tsamba 91 ndime 2 ndi 3, ndiponso tsamba 108 ndi 109. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene tikuphunzirapo.
Nyimbo Na. 56 ndi Pemphero