Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu May ndi June: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena gawirani timapepala totsatirati: Kodi Baibulo Mumalikhulupirira?, Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?, Kodi N’chiyani Chingathandize Kuti Banja Likhale Losangalala?, Kodi Dziko Lapansili Lili M’manja mwa Ndani? kapena kakuti, Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi? July: Gawirani timabuku totsatirati: Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu, Mverani Mulungu ndi kakuti, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha.
◼ August: Tidzakhala ndi ntchito yapadera yogawira kapepala katsopano kodziwitsa anthu za webusaiti yathu ya jw.org/ny.