Zochitika mu Utumiki Wakumunda
Mu November 2013, abale ndi alongo okwana 2,798 anachita upainiya wothandiza. Anthuwa anapangitsa maphunziro a Baibulo okwana 9,330. Izitu zikusonyeza kuti Yehova akutithandiza komanso akudalitsa ntchito yolalikira m’gawo la nthambi yathu.